medische vragenlijst: tract digestivus Flashcards

1
Q

hebt u pijn in uw buik?

A

mukupweteka m’mimba?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
2
Q

voelt u zich misselijk?

A

mukumva nseru?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
3
Q

heeft u last van zuur?

A

muli ndi chinungulira?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
4
Q

krijgt u pijn tijdens het eten?

A

mukumva kupweteka pakudya?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
5
Q

geeft u over na het eten?

A

mukadya mumasanza?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
6
Q

geeft u bloed over?

A

mumasanza magazi?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
7
Q

het u pijn bij het eten of slikken?

A

mumamva kupweteka pakudya kapena kumeza?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
8
Q

zit er bloed bij de ontlasting?

A

mumachita chimbudzi cha magazi?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
9
Q

hebt u constipatie?

A

mumachita chimbudzi cholimba/chouma?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
10
Q

hebt u diarree?

A

m’mimba mumatsegula?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
11
Q

hoe vaak per dag?

A

kangati patsiku limodzi?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
12
Q

hebt u waterig diarree?

A

mukatsekula m’mimba chimbudzi ndi cha madzi?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
13
Q

heeft u bloed bij de diarree?

A

muli magazi m’chimbudzi cha madzi?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
14
Q

zit er bloed bij de ontlasting?

A

muli magazi m’chimbudzi?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
15
Q

ziet u slijm in de ontlasting?

A

mukuona mafinya m’chimbudzi?

How well did you know this?
1
Not at all
2
3
4
5
Perfectly
16
Q

ziet u wormen in de onlasting?

A

mukuona njoka m’chimbudzi?

17
Q

hoort u lawaai in de buik?

A

mumamva kulira m’mimba?

18
Q

laat u winden?

A

mumapwitsa?

19
Q

is de ontlasting erg zwart?

A

chimbudzi ndi chakuda kwambiri?

20
Q

is de pijn branderig?

A

kupweteka kukukuochani?

21
Q

is de pijn stekend?

A

kupweteka kukukulasani?

22
Q

begon de pijn opeens?

A

kupweteka kunayamba mwadzidzidzi?

23
Q

begon de pijn langzaam?

A

kupweteka kunayamba pan’gono pang’ono?

24
Q

hoe lang had u pijn?

A

munamva kupweteka nthawi yanji?

25
toen de pijn begon, werd het erger of minder?
pamene kupweteka kunayamba kunaonjeza kapena kunachepa?
26
hoeveel tijd zit er tussen de aanvallen?
pakati pa kupweteka pamapita nthawi yaitali bwanji?
27
hoe lang duurde de aanvallen?
kupweteka knapitiriza nthawi yanyi?
28
heeft u gele ogen gehad?
munali ndi maso a chikaso?