Time & Numbers Flashcards
1
Q
Sekondi
A
Second
2
Q
Mphindi
A
Minute
3
Q
Ola
A
Hour
4
Q
M’mamawa
A
Morning, really early
5
Q
M’mawa
A
Morning
6
Q
Kutuluka kwa dzuwa
A
Sunrise
7
Q
Masana
A
Noon
8
Q
Madzulo
A
Afternoon, evening
9
Q
Usana / usika
A
Day / night
10
Q
Kulowa kwa dzuwa
A
Sunset
11
Q
Tsiku
A
Day
12
Q
Lero
A
Today
13
Q
Mawa
A
Tomorrow
14
Q
Mkuja
A
Day after tomorrow
15
Q
Mtondo
A
Day after mkuja
16
Q
Dzulo
A
Yesterday
17
Q
Dzana
A
The day before yesterday
18
Q
Mlungu, sabata, wiki
A
Week
19
Q
Lolemba
A
Monday
20
Q
Lachiwiri
A
Tuesday
21
Q
Lachitatu
A
Wednesday
22
Q
Lachinayi
A
Thursday
23
Q
Lachisanu
A
Friday
24
Q
Loweruka
A
Saturday
25
Lamulungu
Sunday
26
Mwezi
Month
27
Chaka
Year
28
Mlungu watha
Last week
29
Mlungu uno
This week
30
Mlungu wamawa / sabata yamawa
Next week
31
MWezi watha
Last month
32
Mwezi uno
This month
33
Mwezi wamawa
Next month
34
Chaka chatha
Last year
35
Chaka chino
This year
36
Chaka chamawa
Next year
37
- modzi
1
38
-wiri
2
39
-tatu
3
40
-nayi
4
41
-sanu
5