Chichewa nouns Flashcards
Munthu / Anthu
Mu / A -
A / A
Человек
Person / People
Mu / A
Mpando / Mipando
Mu / Mi
U / I
Стул
Chair / Chairs
Mu / Mi
Chinthu / Zinthu
Chi / Zi
Chi / Zi
Вещь/вещи
Thing / Things
Chi / Zi
Nyumba / nyumba
I / Zi
I / Zi
Дом
House / houses
I / Zi
Dzina / Maina
Li / Ma
Li / A
Имя
Name / Names
Li / Ma
Ufumu / Maufumu
U / Ma
U / A
Царство
Kingdom / Kingdoms
U / Ma
Bambo / Abambo / Azibambo
Mu / A -
A / A
Отец
Father, Sir, Mr. /
Fathers ( or respectful) /
plural for a group of men
Mu / A
Mayi / Amayi/ Azimayi
Mu / A -
A / A
Мат
Mother or Ms.
plural or respectful
Plural for a group of woman
Mu / A
Mwana/ Ana
Mu / A -
A / A
Ребёнок
Child / children
Mu / A
Mwamuna/ Amuna
Mu / A -
A / A
Человек/муж
Man, husband / men, husbands
Mu / A
Mkazi / Akazi
Mu / A -
A / A
Женщина/жена
Woman, Wife / Women, Wives
Mu / A
M’bale / Abale
Mu / A -
A / A
Брат
Sibling (same sex) / theoretically for brothers
Mu / A
Mlongo / Alongo
Mu / A -
A / A
Сестра
Sibling (opposite sex) / theoretically for sisters
Mu / A -
A / A
Mchimwene / Achimwene
Mu / A -
A / A
Брат
Brother / Brothers
Mu / A
Mulungu / Alungu
Mu / A -
A / A
Бог
God/s
Mu / A -
A / A
Baibulo / Mabaibulo
Li / Ma
Li / A
Библия
Bible/s
Li / Ma
Li / A
Chinthu / Zinthu
Chi / Zi
Chi / Zi
Вещи
Thing/s
Chi / Zi
Chi / Zi
Mu / A
A / A
This class is Generally for people & some animals. However there are exceptions. The singular will often begin with m, mu or mw and is always changed to an A in the plural. With people the noun is often put in the plural to show respect.
Mu / Mi
U / I
The nouns in this class also generally start with m, mu or mw in the singular. They are always changed to Mi in the plural.
Chi / Zi
Chi / Zi
Almost all nouns start with CHI in the singular are in this class. There are very few exceptions. The plural is changed to Zi.
I / Zi
I / Zi
Many nouns in this class start with n, mb, n’g. Note: in this class the plural does not change.
Li / Ma
Li / A
Nouns in this class begin with a variety of letters. You always add a MA for the plural.
U / Ma
U / A
The nouns in this class always begin with U. Adding MA makes the plural of the noun.
English words in a class
Can be confusing. Often in a mixed class. Sometimes singular in the I / Zi class and plural in the Li/ Ma class
Chovala / Zovala
Chi / Zi
Одежда
Clothes
Ulendo / maulendo
U / ma
Поездка
Journey, trip
Banja / mabanja
Li / ma
Семья
Family / families
Bodza / mabodza
Li / ma
Ложь
Lie / s
Msonkhano / misonkhano
Mu / Mi
Встречи
Meeting/s
Pempero / Mapemphero
Li / ma
Prayer/s
Chinsini / zinsinsi
Chi / Zi
Secret/s