Time Flashcards
Tsopano
Now
Padakali pano
Right now
Lero
Today
Tsiku lililonse
Everyday
Mawa
Tomorrow
Dzulo
Yesterday
Mulungu uno
This week
Mulungu watha
Last week
Mulungu wa mawa
Next week
Mulungu ulionse
Every week
Mwezi uno
This month
Mwezi watha
Last month
Mwezi wa mawa
Next month
Mwezi ulionse
Every month
Chaka chino
This year
Chaka chatha
Last year
Chaka cha mawa
Next year
Chaka chilichonse
Every year
Lamulungu
Sunday
Lolemba
Monday
Lachiwiri
Tuesday
Lachitatu
Wednesday
Lachinayi
Thursday
Lachisanu
Friday
Loweruka
Saturday
Mmamawa
Morning
Masana
Noon/afternoon
Madzulo
Evening
Usiku
Night
Nthawi zonse
All the time
Nthawi zina
Some timese
Kawiri Kawiri
Often
Kwambiri
A lot/very much
Pangono
Less/a little
M’mbuyomu
In the past
Kale kale
Long ago
Zara ziwiri zapita zo
Two years ago
Miyezi iwiri yapita yo
Two months ago
Masiku awiri apita wo
Two days ago
Mofulumira
Early
Mochedwa
Late
Mofulumira
Early
Mochedwa
Late