Lesson 16-20 Nouns & Useful Flashcards
Tiyeni
Let’s go/ or let’s do something
Koma
But
Kutali
Far
Kutalitali
Very far
Pafupi
Close
Pafupifupi
Very close/ almost
Kwabasi
Very much, too much
Pepani
Sorry
Njira
Path, way
Njinga
Bicycle
Ndege
Airplane
Ngozi
Accident
Mphatso
Gift
Thumba
Sack, pocket
Moyo
Life, soul
Moto
Fire
Thanzi
Health
Matenda
Sickness
Mankhwala
Medicine
Malungo
Malaria
Mphamvu
Strength, power
Zilonda
Sore
Mabala
Wound
Komabe
However
Kapena
Perhaps
Monga
Like
Ngati
If, as
Pamene
When
Ngakhale
Even, even though
Popeza
Since
Puma
Breathe, rest
Zipatala
Hospitals
Maliro
Funeral
Malonda
Sale, trade
Ngongole
Debt
Mchere
Salt
Chidwi
Interest
Chikwama
Zikwama
Purse, bag
Mzungu
White
Mmwenye
Indian
Msilikali
Soldier
Mfuti
Gun, rifle
Nkhondo
War, fight
Ndewu
Quarrel fight.
Mtendere
Peace
Chuma
Riches, wealth
Denga
Roof
Dengu
Large basket
Dothi
Dirt, ground
Nthaka
Earth, land, soil