Lesson 13 Flashcards
supposed to
yenera
repair/mend
konza
where are you?
muli kuti?
I am at home
ndili pakhomo
chairs
mipando
I want to buy chairs
ndikufuna kugula mipando
near / close / short
pafupi
road
msewu
door
chitseko
take
tenga
string / rope
chingwe
you can be able to
mungathe
I can go
ndingapite
I am able to drive a car
ndimatha kuyendetsa galimoto
you sleep well
mugone bwino
can you eat pork
mungadye nkhumba
he didn’t go to work
sanapite kuntchito
things
zinthu
a thing
chinthu
basket
dengu
in there
umo
throw away / get rid of
taya
throw to someone to catch it
ponya
on there
apo
at over there
uko
the direction you are facing
uku
a little
pang’ono
I am very good
ndili bwino bwino
my / mine
nga
our
thu
his / hers
ke
your(s)
nu / ko
their
wo
land / country
dziko
in the same house
m’nyumba imodzi
my own car
galimoto yangayanga
his own car
galimoto yakeyake
our own car
galimoto yathuyathu
at (possession)
kwa
I am going to my place
ndikupita kwanga
wound
chilonda
flowers
maluwa
here
pano
I am not hungry
ndilibe njala
I am not a child
sindine mwana
cry
lira
funeral / death has fallen
kunegwa maliro
anything
kanthu