Chichewa Language Flashcards
Hello
Moni
What’s up?
Zikuyenda bwanji?
Nothing special
Palibe chapadera
You are how? (How are you?)
Muli bwanji?
I’m okay and you?
Ndili bwino kaya inu?
You are most welcome
Mwalandilidwa
See you later
Tiwonana
Thanks
Zikomo
Sorry
Chonde pepani
You woke up how? (How did you wake up?)
Mwadzuka bwanji?
I woke up well, what about you?
Ndadzuka bwino kaya inu?
I woke up well too thank you
Ndadzuka bwinonso zikomo
You spent the day how?
Mwaswela bwanji?
I spent the day well, what about you?
Ndaswela bwino kaya inu?
I spent the day well too, thank you
Ndaswela bwinonso zikomo
How was the night?
Usiku unali bwanji?
The night was good thank you
Usiku unali bwino zikomo
How was the day?
Tsiku linali bwanji?
The day was good thank you
Tsiku linali bwino zikomo
How is your father?
Abambo anu ali bwanji?
My father is fine thanks
Abambo anga ali bwino zikomo
What is your name?
Dzina lanu ndani
My name is Kyla and yours?
Dzina langa ndi Susan
Happy to meet you
Ndakondwa kukumana ndi inu
Happy to meet you too
Ndakondwa kukumananso ndi inu
Where are you from?
Mumachokera kuti?
I am from USA
Ndimachokera ku USA
What is your job?/What do you do?
Mumagwira ntchito yanji?
I do work of a volunteer
Ndimagwira ntchito yodzipereka
I learning to speak Chichewa
Ndikuphunzira kulankhula Chichewa
Where will you stay?
Mudzakhala kuti?
I will stay in Dedza
Ndidzakhala ku Dedza
Thanks see you later
Zikomo tiwonana
Family
Banji
Father
Bambo
Mother
Mayi
Brother
Achimwene
Sister
Achemwali
Grandfather
Agogo amuna
Grandmother
Agogo akazi
Children
Ana
To be married
Kukwatira/kukwatiwa
Single child
Mwana m’modzi
Twins
Mapasa
Boy/girlfriend
Chibwenzi
My friend
Mzanga
To be separated
Kulekana
To have
Kukhala ndi
Uncle
Amalume
Aunt
Azakhali
How is your family?
Banja lanu lili bwanji?
Our family is fine thank you
Banja lathu lili bwino zikomo
I am tired
Ndatopa
I am hungry
Ndili ndi njala
I am full
Ndakhuta
I am thirsty
Ndili ndi ludzu
Where is the toilet?
Chimbudzi chili kuti?
I want to drink water
Ndikifuna kumwa madzi
I want to sleep
Ndikufuna kugona
I want to eat
Ndikufuna kudya
I am feeling hot
Ndikumva kutentha
I am feeling cold
Ndikumva kuzizira
Toilet
Chimbudzi
Shower room
Bafa
I want to bathe
Ndikufuna kusamba
I don’t like meat
Sindimakonda nyama
How do you say…in Chichewa?
Mumati chiyani…mu Chichewa?
Yes
Inde
No
Iyayi/Ayi
Who?
Ndani?
Where?
Kuti?
What?
Chiyani?
How many?
Angati?
What time?
Nthawi yanji?
When?
Liti?
How much?
Ndalama zingati?
Why?
Chifukwa chiyani?
How?
Bwanji?
Because
Chifukwa
Please eat
Idyani
Please sit
Khalani
Come here
Bwerani kuno
Please wait
Dikirani
Let’s go/come on
Tiyeni
False/untrue
Bodza
True
Zowona
That’s enough
Basi
Do you understand?
Mukumvetsa?
I need (coke) please
Ndikufuna (coke) chonde
Give me (water) please
Ndipatseni madzi chonde
Go well
Pitani bwino
Stay well
Tsalani bwino
One
Modzi
Two
Wiri
Three
Tatu
Four
Nayi
Five
Sanu
Six
Sanu ndi modzi
Seven
Sanu ndi wiri
Eight
Sanu ndi tatu
Nine
Sanu ndi nayi
Ten
Khumi
Food
Chakudya
Rice
Mpunga
Side dishes
Ndiwo
Meat
Nyama
Pork
Nyama ya nkhumba
Beef
Nyama ya ng’ombe
Chicken
Nkhuku
Fish
Nsomba
Eggs
Mazira
Greens
Masamba
Beans
Nyemba
Peanut butter
Chiponde
Peanut
Mtedza
Oil
Mafuta
Salt
Mchere
Pepper
Tsabola
Irish potatoes
Mbatatesi
Sweet potatoes
Mbatata
Tomato
Matimati
Pumpkin leaves
Masamba a nkhwani
Pigeon peas
Msawawa
Fruits
Zipatso
Paw paw
Papaya
Pineapple
Chinananzi
Mango
Mango
Cassava
Chinangwa
Corn
Chimanga
Cucumber
Nkhaka
Drinks
Zakumwa
Water
Madzi
Rice-water
Madzi a mpunga
Tea
Tiyi
Beer
Mowa
Milk
Mkaka
Monday
Lolemba
Tuesday
Lachiwiri
Wednesday
Lachitatu
Thursday
Lachinayi
Friday
Lachisanu
Saturday
Loweluka
Sunday
Lamulunga
Yesterday
Dzulo
Today
Lero
Tomorrow
Mawa
Morning
M’mawa
Noon
Masana
Evening
Usiku
That makes me happy
Chimandisangalatsa
That’s sad
Zomvetsa chisoni
That’s surprising
Zodabwitsa
That’s shocking
Zochititsa mantha
It’s tiring
Zotopetsa
That’s annoying
Zokwiyitsa
That’s doubtful
Zokayikitsa
He/She is happy.
Ndiwosangalala
You are surprised
Muli wodabwa
I am sad
Sindili wosangalala
They are afraid
Ali ndi mantha
He/she is lazy
Ndiwaulesi
I hate it
Ndimadana nazo
I trust you
Ndimakukhulupilira
Chair
Mpando
Table
Tebulo
Bed frame
Kama
Blankets
Zofunda
Door
Chitseko
Window
Zenera
Mosquito net
Chotetezera udzudzu
Mat
Mphasa
Broom
Tsache
Hello mother
Moni mayi
Hello father
Moni bambo
Good morning
Mwadzuka bwanji
Thank you see you later
Zikomo tiwonana
What about
kaya
Come
Bwera
This
Ichi
Honey
Uchi
Farming
Ulimi
Little
Pang’ono
Look
Yang’ana
To be dangerous
Kuwopsya
Disease/diseases
Nthenda/Matenda
To discuss
Kukambirana
To talk
Line a
Broom
Mseso
Mistake
Ulakwitza
Menstruation
Kukula chinamwali
Group
Gulu
Animal
Chin’yama
To be tamed
Kusungidwa or Kuwetedwa
Long
-tali
Pointed
-itali
Everything
Chilichonse/Zilizonse
To try
Kuyesa
To look like or to appear to look like
Kuoneka
To be like; To look like; To be alike; To be equal or the same
Kufanana
Jealousy
Njiru
To guard
Kulondera
To protect
Kuchinjiriza
Place
Malo
Thief
Mbava
Boss
Bwana; Mbuye
To be loved or liked
Kukondedwa
Example
Chitsanzo/Zitsanzo
Word
Mau
To kill
Kupha
To break (out of anger/into pieces)
Kuphwanya
To be expensive; To cut (trees; into parts)
Kudula
To be fat
Kunenepa
To be swollen
Kutupa
To be malnourished
Kunyentchera
And also
Ndinso
What is it?
Ndi yanji?
Short - Njanji?
Canoe
Bwato
Between
Pakati
Meeting
Msonkhano/Misonkhano
To start
Kuyambitsa
Friend
Mnza/Anza
Road
Mseyu/Miseyu
Arrow
Muvi/Mivi
Big; very important
-kulu
The truth
Choona/Zoona
Blanket
Chofunda
Zatheka
It is successful.
To change
Kusintha
Leader
Utsogoleri
To wonder
Kudabwa
A person you can depend on
Mwala wa mthunzi
Forever
Mpaka kalekale
Until
Mpaka
Word
Mau
Number
Nambala
Earthquake
Chivomezi
Another (person)
Wina
Answer
Yankho
Better
Bola
Mushroom
Bowa
Basket
Dengu
Bar
Bala
Dress
Dilesi
Wall
Khoma
To hammer, hit
Kukhoma
Foam, lather, bubbles
Thovu
Keep going, don’t lose heart
Pirirani
Bush, wild area
Tchire
Tent
Hema
Gift
Mphatso
Hippo
Mvuu
Brick
Njerwa
Rib
Nthiti
Darkness
Mdima
Lip
Mlomo
Neighbor
Mnansi
Spirit
Mzimu
Native Doctor, medicine man
Sing’anga
To be ripe or fully cooked
Kupsa
Chance, opportunity
Mwayi
To stay
Kutsala
To climb/hike
Kukwera
To scold
Kukalipira
To fail
Kulepera
Time is up/against us
Nthawi sikuti lola
Mostly
Kweni kweni
Especially
Maka maka
To be used to doing something
Kuzolowera
Have a good weekend
Kukhale ndi mapeto asabata a bwino
To refuse
Kukhana
To lie
Kunama
To shout, to scold
Kukalipira
To be busy
Kutanganidwa
Only
Yokha