Chichewa Flashcards
Eya
Yes
Yes
Eya, Ee! Inde
Ee!
Yes
Inde
Yes
Mono
Hello
Nonse
Everybody, everyone
Zikomo
Thank you/ excuses me
Zikomo Kwambiri
Thanks a lot, thank you very much
Pepani
Sorry, I’m sorry
Pepani kwambiri
I am really sorry
Muli bwanji
How are you!
Uli bwanji
How are you (junior)
Ndiri bwino
I am fine, I am well, I am alright
Tiri bwino
We are good (in a group)
Ndiri bwino kanya inu
I am well, how about you?
Inu
You (respect)
Iwe
You (no respect required)
Inuyo?
You?
Ndikudwala
I am sick
Mukudwala Chiyani?
What are you sick from? What the problem?
Sindiri bwino
I am not well
Vuto ndi chiyani
What is the problem
Dzina ianu ndani
What is your name
Ndinu ndani
Who are you?
Dzina Langa ndi
My name is
Kuyambira kuti
Where do you stay?
Dzina langa ndi
My name is
Ndimakhala ku
I stay in
Ine ndi kufuna
I want
Madzi
Water
Kodi mungandithandize ndi
Can you help me with
Ndalama zosezo
All that much?
Ndalama zingati?
How much money?
Ichi ndi chiyani mu chichewa?
What do you call this in Chichewa